1 Mbiri 12:21 BL92

21 Ndipo anathandiza Davide aponyane nalo gulu la acifwamba, pakuti onse ndiwo ngwazi zamphamvu, nakhala atsogoleri m'khamu la nkhondo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 12

Onani 1 Mbiri 12:21 nkhani