1 Mbiri 12:29 BL92

29 Ndi a ana a Benjamini, abale a Sauli, zikwi zitatu; pakuti mpaka pomwepo ocuruka a iwowa anaumirira nyumba ya Sauli.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 12

Onani 1 Mbiri 12:29 nkhani