30 Ndi a ana a Efraimu zikwi makumi awiri mphambu mazana asanu ndi atatu, ngwazi zamphamvu, anthu omveka m'nyumba za makolo ao.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 12
Onani 1 Mbiri 12:30 nkhani