31 Ndipo a pfuko la Manase logawika pakati zikwi khumi mphambu zisanu ndi zitatu, ochulidwa maina ao kuti adzalonge Davide mfumu.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 12
Onani 1 Mbiri 12:31 nkhani