1 Mbiri 12:32 BL92

32 Ndi a ana a Isakara, anthu akuzindikira nyengo, akudziwa zoyenera Israyeli kuzicita, akuru ao ndiwo mazana awiri; ndi abale ao onse anapenyerera pakamwa pao.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 12

Onani 1 Mbiri 12:32 nkhani