34 Ndi a Nafitali atsogoleri cikwi cimodzi, ndi pamodzi nao ogwira zikopa ndi mikondo zikwi makumi atatu mphambu zisanu ndi ziwiri.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 12
Onani 1 Mbiri 12:34 nkhani