1 Mbiri 12:37 BL92

37 Ndi tsidya lga la Yordano a Arubeni, ndi Agadi, ndi pfuko la: Manase logawika pakati, ndi zida: ziri zonse za khamu kucita nazo nkhondo, zikwi zana limodzi ndi makumi awiri.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 12

Onani 1 Mbiri 12:37 nkhani