1 Mbiri 12:38 BL92

38 Onsewa, ndiwo anthu a nkhondo akusunga malongosoledwe a nkhondo, anadza ku Hebroni ndi mtima wangwiro kudzamlonga Davide mfumu ya Aisraeli onse; ndi onse otsala a Israyeli omwe anali a mtima umodzi kumlonga Davide ufumu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 12

Onani 1 Mbiri 12:38 nkhani