1 Mbiri 14:1 BL92

1 Ndipo Hiramu mfumu ya Turo anatumiza mithenga kwa Davide, ndi mikungudza, ndi amisiri omanga miyala, ndi amatabwa, kuti ammangire nyumba.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 14

Onani 1 Mbiri 14:1 nkhani