1 Mbiri 14:2 BL92

2 Ndipo Davide anazindikira kuti Yehova adamkhazikitsa mfumu ya Israyeli; pakuti ufumu wace unakwezekadi, cifukwa ca anthu ace Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 14

Onani 1 Mbiri 14:2 nkhani