1 Mbiri 14:10 BL92

10 Ndipo Davide anafunsira kwa Mulungu, kun, Ndikwere kodi kuyambana ndi Afilisti? mudzawapereka m'dzanja langa kodi? Ndipo Yehova anati kwa iye, Kwera, pakuti ndidzawapereka m'dzanja lako.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 14

Onani 1 Mbiri 14:10 nkhani