1 Mbiri 14:11 BL92

11 Atafika tsono ku Baala Perazimu, Davide anawakantha komweko; nati Davide, Mulungu anapasula adani anga ndi dzanja langa, ngati pokhamulira madzi. Cifukwa cace analicha dzina la malowo Baala Perazimu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 14

Onani 1 Mbiri 14:11 nkhani