1 Mbiri 14:14 BL92

14 Ndipo Davide anafunsiranso kwa Mulungu, nanena Mulungu naye, Usakwera kuwatsata, uwazungulire, nuwadzere pandunji pa mitengo ya mkandankhuku.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 14

Onani 1 Mbiri 14:14 nkhani