1 Mbiri 14:15 BL92

15 Ndipo kudzali, pakumva iwe kuwayula kunsonga kwa mitengo ya mkandankhuku, pamenepo uturukire kunkhondo; pakuti Mulungu waturukira pamaso pako kukantha gulu la Afilisti.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 14

Onani 1 Mbiri 14:15 nkhani