1 Mbiri 15:1 BL92

1 Ndipo Davide anadzimangira nyumba m'mudzi mwace, nakonzeratu malo likasa la Mulungu, naliutsira hema.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 15

Onani 1 Mbiri 15:1 nkhani