1 Mbiri 15:2 BL92

2 Pamenepo Davide anati, Sayenera ena kusenza likasa la Mulungu koma Alevi ndiwo; pakuti Yehova anawasankha iwo kusenza likasa la Mulungu, ndi kumtumikira iye kosatha.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 15

Onani 1 Mbiri 15:2 nkhani