1 Mbiri 15:15 BL92

15 Ndipo ana a Alevi anasenza likasa la Mulungu pa mapewa ao, mphiko ziri m'mwemo, monga Mose anawauza, monga mwa mau a Yehova.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 15

Onani 1 Mbiri 15:15 nkhani