1 Mbiri 15:16 BL92

16 Ndipo Davide ananena ndi mkuru wa Alevi kuti aike abale ao oyimbawo ndi zoyimbira, zisakasa, ndi azeze, ndi nsanje, azimveketse ndi kukweza mau ao ndi cimwemwe.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 15

Onani 1 Mbiri 15:16 nkhani