28 Momwemo Aisrayeli onse anakwera nalo likasa la cipangano la Yehova ndi kupfuula, ndi kumveka kwa lipenga, ndi mphalasa, ndi nsanje zomveketsa, ndi zisakasa, ndi azeze.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 15
Onani 1 Mbiri 15:28 nkhani