1 Mbiri 15:29 BL92

29 Ndipo polowa likasa la cipangano la Yehova m'mudzi wa Davide, Mikala mwana wamkazi wa Sauli anasuzumira pazenera, naona mfumu Davide alikutumphatumpha ndi kusewera; ndipo anampeputsa mumtima mwace.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 15

Onani 1 Mbiri 15:29 nkhani