1 Mbiri 16:35 BL92

35 Nimunene, Tipulumutseni, Mulungu wa cipulumutso cathu;Mutisokolotse ndi kutilanditsa kwa amitundu,Kuti tiyamike dzina lanu loyera,Ndi kudzitamandira naco cilemekezo canu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 16

Onani 1 Mbiri 16:35 nkhani