36 Alemekezedwe Yehova Mulungu wa Israyeli,Kuyambira kosayamba kufikira kosatha.Ndipo anthu onse anati, Amen! nalemekeza Yehova.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 16
Onani 1 Mbiri 16:36 nkhani