1 Mbiri 17:1 BL92

1 Ndipo pokhala Davide m'nyumba mwace, Davideyo anati kwa Natani mneneri, Taona, ndikhala ine m'nyumba yamikungudza, koma Gkasa la cipangano likhala m'nsaru zocinga.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 17

Onani 1 Mbiri 17:1 nkhani