1 Mbiri 17:11 BL92

11 Ndipo kudzacitika, atakwanira masiku ako kuti uzipita kukhala ndi makolo ako, ndidzaukitsa mbeu yako pambuyo pako, ndiye wa ana ako; ndipo ndidzakhazikitsa ufumu wace.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 17

Onani 1 Mbiri 17:11 nkhani