10 ndi kuyambira kuja ndinaika oweruza ayang'anire anthu anga Israyeli; ndipo ndagonjetsa adani ako onse. Ndikuuzanso kuti Yehova adzakumangira banja.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 17
Onani 1 Mbiri 17:10 nkhani