1 Mbiri 17:9 BL92

9 Ndipo ndaikira anthu anga Israyeli malo, ndi kuwaoka, kuti akhale m'malo mwao osasunthikanso; ndi ana osalungama sadzawapululanso monga poyamba paja;

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 17

Onani 1 Mbiri 17:9 nkhani