1 Mbiri 17:17 BL92

17 Ndipo ici ncacing'ono pamaso panu, Mulungu, koma mwanena za nyumba ya mtumiki wanu nthawi yam'tsogolo ndithu, ndipo mwandiyesera ngati munthu womveka, Yehova Mulungu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 17

Onani 1 Mbiri 17:17 nkhani