16 Pamenepo mfumu Davide analowa nakhala pamaso pa Yehova, nati, Ndine yani, Yehova Mulungu, ndi nyumba yanga njotani kuti mwandifikitsa mpaka pano?
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 17
Onani 1 Mbiri 17:16 nkhani