1 Mbiri 17:25 BL92

25 Pakuti Inu, Mulungu wanga, mwaululira mtumiki wanu kuti mudzammangira banja; momwemo mtumiki wanu waona mtima wakupemphera pamaso panu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 17

Onani 1 Mbiri 17:25 nkhani