1 Mbiri 17:7 BL92

7 Cifukwa cace tsono, uzitero naye mtumiki wanga Davide, Atero Ambuye wa makamu, Ndinakutenga kubusa potsata iwe nkhosa, kuti ukhale mtsogoleri wa anthu anga Israyeli;

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 17

Onani 1 Mbiri 17:7 nkhani