1 Mbiri 18:14 BL92

14 Ndipo Davide anakhala mfumu ya Aisrayeli onse, naweruza anthu ace onse, nawacitira cilungamo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 18

Onani 1 Mbiri 18:14 nkhani