1 Mbiri 18:15 BL92

15 Ndipo Yoabu mwana wa Zeruya anayang'anira khamu la nkhondo, ndi Yehosafati mwana wa Ahiludi anali wolemba mbiri.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 18

Onani 1 Mbiri 18:15 nkhani