10 Pakuona Yoabu tsono kuti nkhondo inamdzera kumaso ndi kumbuyo, anasankha amuna osankhika onse a Israyeli, nawanika ayambane ndi Aaramu.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 19
Onani 1 Mbiri 19:10 nkhani