9 Ndipo ana a Amoni anaturuka, nandandalitsa nkhondo ku cipata ca mudzi, ndi mafumu adadzawo anali pa okha kuthengo.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 19
Onani 1 Mbiri 19:9 nkhani