15 Ndipo pakuona ana a Amoni kuti adathawa Aaramu, iwo omwe anathawa pamaso pa Abisai mbale wace, nalowa m'mudzi. Pamenepo Yoabu anadza ku Yerusalemu.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 19
Onani 1 Mbiri 19:15 nkhani