16 Ndipo pakuona Aaramu kuti Israyeli anawakantha, anatumiza mithenga, naturuka nao Aaramu akukhala tsidya lija la mtsinjewo; ndi Sofaki kazembe wa khamu la Hadarezeri anawatsogolera.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 19
Onani 1 Mbiri 19:16 nkhani