18 Ndipo Aaramu anathawa pamaso pa Israyeli; ndipo Davide anapha Aaramu apamagareta zikwi zisanu ndi ziwiri, ndi oyenda pansi zikwi makumi anai; napha Sofaki kazembe wa khamulo.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 19
Onani 1 Mbiri 19:18 nkhani