1 Mbiri 19:19 BL92

19 Ndipo pakuona anyamata a Hadarezeri kuti Israyeli anawakantha, anapangana mtendere ndi Davide, namtumikira; ndi Aaramu anakana kuthandizanso ana a Amoni.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 19

Onani 1 Mbiri 19:19 nkhani