1 Mbiri 21:20 BL92

20 Poceuka Orinani anaona wamthengayo; ndi ana ace amuna anai anali naye anabisala. Koma Orinani analikupuntha tirigu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 21

Onani 1 Mbiri 21:20 nkhani