1 Mbiri 21:21 BL92

21 Ndipo pofika Davide kwa Orinani, Orinaniyo anapenyetsa, naona Davide, naturuka kudwale, nawerama kwa Davide, nkhope yace pansi.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 21

Onani 1 Mbiri 21:21 nkhani