22 Davide tsono anati kwa Orinani, Ndipatse padwale pano kuti ndimangepo guwa la nsembe la Yehova; undipatse gi pa mtengo wace wonse, kuti mliri ulekeke pa anthu.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 21
Onani 1 Mbiri 21:22 nkhani