24 Koma mfumu Davide anati kwa Orinani, lai, koma ndidzaligula pa mtengo wace wonse; pakuti sindidzatengera Yehova ciri cako, kapena kupereka nsembe yopsereza yopanda mtengo wace.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 21
Onani 1 Mbiri 21:24 nkhani