1 Mbiri 22:10 BL92

10 iyeyu adzamangira dzina langa nyumba; iye adzakhala mwana wanga, ndi Ine ndidzakhala Atate wace; ndipo ndidzakhazikitsa mpando wacifumu wa ufumu wace pa Israyeli kosalekeza.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 22

Onani 1 Mbiri 22:10 nkhani