1 Mbiri 23:17 BL92

17 Ndi ana a Eliezeri: wamkuru ndi Rehabiya. Ndipo Eliezeri analibe ana ena, koma ana a Rehabiya anacuruka kwambiri.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 23

Onani 1 Mbiri 23:17 nkhani