1 Mbiri 24:3 BL92

3 Ndipo Davide pamodzi ndi Zadoki wa ana a Eleazara, ndi Ahimeleke wa ana a Itamara, anawagawa, monga mwa malongosoledwe ao m'utumiki wao.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 24

Onani 1 Mbiri 24:3 nkhani