1 Mbiri 24:4 BL92

4 Ndipo anapeza kuti amuna akuru a ana a Eleazara anacuruka, a ana a Itamara anacepa; nawagawa motero: pa ana a Eleazara panali khumi mphambu asanu ndi mmodzi, akuru a nyumba za makolo; ndi pa ana a Itamara, monga mwa nyumba za makolo ao, panali asanu ndi atatu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 24

Onani 1 Mbiri 24:4 nkhani