1 Mbiri 24:5 BL92

5 Ndipo anawagawa ndi maere, awa ndi aja; pakuti panali akalonga a malo opatulika, ndi akalonga a kwa Mulungu, a ana a Eleazara ndi a ana a Itamara omwe.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 24

Onani 1 Mbiri 24:5 nkhani