31 Awanso anacita maere monga abale ao ana a Aroni, pamaso pa Davide mfumu, ndi Zadoki, ndi Ahimeleki, ndi akuru a nyumba za makolo za ansembe ndi Alevi; mkuru wa nyumba za makolo monga mng'ono wace.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 24
Onani 1 Mbiri 24:31 nkhani