2 a ana a Asafu: Zakuri, ndi Yosefe, ndi Netaniya, ndi Asarela, ana a Asafu; mwa cilangizo ca Asafu, wakunenera mwa cilangizo ca mfumu.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 25
Onani 1 Mbiri 25:2 nkhani