1 Mbiri 25:5 BL92

5 awa onse ndiwo ana a Hemani mlauli wa mfumu m'mau a Mulungu, kuti akweze mphamvu yace. Ndipo Mulungu anapatsa Hemani ana amuna khumi ndi anai, ndi ana akazi atatu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 25

Onani 1 Mbiri 25:5 nkhani